Woman dumps her child at police station to save marriage with new husband.

Amai ndi ana awa ali mu chitikosi cha police kwa Manase, blantyre.

Amaiwo anali ndi ana awiri asanapeze banja, atalipeza amuna awo atsopanowa anamuuza kuti ana ake sakuwafuna.

maiwo mwana Ali mmanja mwao abereka ndi mwana watsopano.

Mwana wamkuluyo anakamutaya pa police ya Manase,blantyre wina wa mkaziyo ocheperakoyo anamusiya kwa amai ena kuti akhale wawo, panopa Ali mmanja mwa Police.

Subscribe to AIH whatsapp forum for more News Updates 0998376011

%d bloggers like this: