[Watch] Angry lilongwe residents destroy SR Nicholas construction company brick fense after city council allocated the space for a market.

…Pagawidwa malo pa area 3 near mbc next to madzi house,malowo akuti anthu amangepo ma buildings kuti ukhale nsika koma usiku panabwera grader yagumulapo zonse zomwe zidamangidwazo akuti city idalakwitsa kupatsa anthu malowo, anthu wokwiya atseka nseu wopita ku chinsapo.

Subscribe to AIH whatsapp forum for more News Updates +265998376011

Leave a Reply

%d bloggers like this: