Mzimayi wina wapha nkumuboola maso mkazi nzake ku Rumphi

Anthuwa anali pa mitala, Mkazi wamkuluyi ndi mwana wake anapita kupanga attack mkazi wamng’ono kunyumba kwake.

Amuna awo anali atapita kogileda fodya.

Chifukwa choti akazi awiriwa samaoneka ku ntchitoko this caused an alarm pakati pa anthu alimi amene amagwira ntchito yogileda fodya.

Anaphera mnyumba, nkumuboola maso, mpaka kumukokela ku tchire kumubisa.

Sent in by AIH whatsapp member.

Subscribe to AIH whatsapp forum for more News Updates +265998376011

%d bloggers like this: