Msilikali waku Kamuzu Barracks wamwalira Galimoto yomwe amaendetsa itagudubuzika.


Msilikali mmodzi Ku Kamuzu BARRACKS wamwalira Galimoto yomwe amaendetsa itagudubuzika pamene amalowa Ku chipata cha KAMUZU BARRACKS

Galimoto yomwe # yake ndi LA 6886 munali anthu okwana 4.

malipoti akusonyeza kuti galimoto imeneyi imathamanga kwambiri zimene zinapangitsa kut Driver akanike kuongolera bwinobwino.

%d bloggers like this: