Mkazi amenyetsa apachibale

Wamenyedwa: Lezo

Malawi mnyamata wakale osewera mpira Lezo Malunga wamenyedwa ndi young brother wake Cecil Malunga.

Malipoti pa social media akuti Lezo anafunsira mkazi wabale wake yemwe anafikitsa nkhaniyi kwa mamuna wake.

Izi zinamukwiyitsa kwambiri Cecil yemwe anamenya ngati akupinda galimoto.

Lezo anathamangitsidwa ku dziko la America ndikutumizidwa kuno kumudzi miyezi itatu yapitayo atangotuluka ku ndende komwe anakhalako zaka zisanu.

Yamikani Chezani

Journalist by profession, I like what I do here, that is, keeping the world close to news As It Happens.

%d bloggers like this: