Fisi wolusa avulaza anthu ku Salima

Anthu atata avulazidwa ndi fisi olusa lero mmawa mmudzi mwa Mbuna, T/A Maganga m’boma LA Salima

Fisiyu anapezana ndi mayi wachikulire pafupifupi dzaka 57 ndipo wadula ndikudya manja onse awiri

Sanalekere pomwepo mnyamata yemwe amati atetedze mayiwa fisiyu anathamangira kudula chitendeni chakumanja .

Bambo nayenso kuti athandidzire wavuladzidwa koopsa

Pakadali piano fisiyu waphedwa ndimunthu wina yemwe amapulumutsa mwana wake fisiyu atafunanso kulikwira mwanayo.

Yamikani Chezani

Journalist by profession, I like what I do here, that is, keeping the world close to news As It Happens.

%d bloggers like this: